Intro Ine ndili desperate for your Love Ine ndili desperate for your hand Ine ndili desperate for your touch Ine ndili desperate, deperate for You verse 1 Chilichonse chomwe ndili nacho chachokera kwa inu Ngakhale ntchito yomwe tikugwirayi timayamika inu Sukulu yonse yomwe taphunzirayi timayamika inu Ngakhale magitala tikuimbawa timayamika inu Ine ndili desperate for your Love Ine ndili desperate for your hand Ine ndili desperate for your touch Ine ndili desperate, x2 Chorus Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Verse2 Chilichonse chomwe ndidzachite ndidzatumikira inu Ngakhale nyimbo zomwe ndidzaimbe, ndidzaimbira inu Mtim wanga thupi langa zones, zidzatumikira inu Ndikufuna mbuye mukamandiona, mudzingomwetulira Ine ndili desperate for your Love Ine ndili desperate for your hand Ine ndili desperate for your touch Ine ndili desperate, x2 Chorus Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Bridge Nthawi zonse ndimafuna, Kuyenda nanu Chikondi chanu chinazula Mtima wanga Mukandiona ndikukwera phiri, kukapemphera, ndili desperate Ngakhale ndimayenda Mnthunzi wa imfa Sindidzaopa poti mbuye, Mulinane Chibonga chanu n?ndodo yanu zindisangalatsa, Ine ndili desperate for your Love Ine ndili desperate for your hand Ine ndili desperate for your touch Ine ndili desperate, desperate for you! For you, for you Ndili desperate for you For you, for you Ine ndili desperate for you For you, for you ending Ndikufuna Nkhope yanu Mbuye, Ndikufuna nkono chanu Mbuye Ndikufuna dzanja lanu mbuye, Edipo ndili desperate, Ndikufuna zozizwa zanu mbuye, Ndikufuna chiyero chanu mbuye Ndikufuna dzanja lanu mbuye, Edipo ndili desperate, Desperate for you

Watch the song video
Top songs from Faith Mussa